Aefeso 2:19, 20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho, si inunso anthu osadziwika kapena alendo,+ koma mofanana ndi oyerawo inunso ndinu nzika+ ndipo ndinu a mʼbanja la Mulungu.+ 20 Mwamangidwa pamaziko a atumwi ndi aneneri+ ndipo Khristu Yesu ndi mwala wapakona wa mazikowo.+
19 Choncho, si inunso anthu osadziwika kapena alendo,+ koma mofanana ndi oyerawo inunso ndinu nzika+ ndipo ndinu a mʼbanja la Mulungu.+ 20 Mwamangidwa pamaziko a atumwi ndi aneneri+ ndipo Khristu Yesu ndi mwala wapakona wa mazikowo.+