Luka 22:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Tsopano amuna amene anagwira Yesu aja anayamba kumuchitira zachipongwe,+ ndi kumumenya.+