Yesaya 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Msana wanga ndinaupereka kwa ondimenya, ndipo masaya anga+ ndinawapereka kwa ozula ndevu. Nkhope yanga sindinaitchinjirize kuti isachitidwe zinthu zamanyazi ndi kulavuliridwa.+ Yesaya 53:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+ Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Chilango chotibweretsera mtendere chinam’gwera iyeyo,+ ndipo chifukwa cha zilonda zake+ ifeyo tachiritsidwa.+ Mateyu 26:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Kenako anayamba kumulavulira kunkhope+ ndi kum’menya+ nkhonya. Ena anamuwomba mbama,+ Maliko 14:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pamenepo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope ndi kumukhoma nkhonya. Iwo anali kunena kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali a pakhoti anamutenga.+
6 Msana wanga ndinaupereka kwa ondimenya, ndipo masaya anga+ ndinawapereka kwa ozula ndevu. Nkhope yanga sindinaitchinjirize kuti isachitidwe zinthu zamanyazi ndi kulavuliridwa.+
5 Iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+ Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Chilango chotibweretsera mtendere chinam’gwera iyeyo,+ ndipo chifukwa cha zilonda zake+ ifeyo tachiritsidwa.+
65 Pamenepo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope ndi kumukhoma nkhonya. Iwo anali kunena kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali a pakhoti anamutenga.+