Mateyu 26:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Kenako anayamba kumulavulira kunkhope+ ndi kum’menya+ nkhonya. Ena anamuwomba mbama,+ Maliko 14:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pamenepo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope ndi kumukhoma nkhonya. Iwo anali kunena kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali a pakhoti anamutenga.+
65 Pamenepo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope ndi kumukhoma nkhonya. Iwo anali kunena kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali a pakhoti anamutenga.+