Maliro 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Aperekere tsaya lake kwa munthu amene akumumenya.+ Alandire chitonzo chokwanira.+ Mika 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Iwe mzinda wogonjetsedwa, tsopano udzichekecheke.+ Adani atizungulira kuti atiukire.+ Iwo adzamenya woweruza wa Isiraeli patsaya ndi ndodo.+ Luka 22:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Tsopano amuna amene anagwira Yesu aja anayamba kumuchitira zachipongwe,+ ndi kumumenya.+ Yohane 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atanena zimenezi, mmodzi wa alonda amene anaimirira chapafupi anamenya Yesu mbama,+ ndi kunena kuti: “Ungamuyankhe choncho wansembe wamkulu?”
5 “Iwe mzinda wogonjetsedwa, tsopano udzichekecheke.+ Adani atizungulira kuti atiukire.+ Iwo adzamenya woweruza wa Isiraeli patsaya ndi ndodo.+
22 Atanena zimenezi, mmodzi wa alonda amene anaimirira chapafupi anamenya Yesu mbama,+ ndi kunena kuti: “Ungamuyankhe choncho wansembe wamkulu?”