Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 50:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Msana wanga ndinaupereka kwa ondimenya, ndipo masaya anga+ ndinawapereka kwa ozula ndevu. Nkhope yanga sindinaitchinjirize kuti isachitidwe zinthu zamanyazi ndi kulavuliridwa.+

  • Mateyu 5:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Koma ine ndikukuuzani kuti: Usalimbane ndi munthu woipa, koma wina akakumenya mbama patsaya lakumanja,+ umutembenuzirenso linalo.

  • Yohane 19:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo anayamba kubwera kwa iye ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!” Komanso anali kumumenya mapama.+

  • Machitidwe 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Atamva zimenezi Hananiya mkulu wa ansembe, analamula anthu amene anaimirira pafupi naye kuti amubwanyule+ pakamwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena