1 Mafumu 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Zedekiya mwana wa Kenaana anayandikira Mikaya ndipo anam’menya mbama,+ n’kunena kuti: “Kodi mzimu wa Yehova wachoka bwanji kwa ine n’kukalankhula ndi iwe?”+ Yeremiya 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya+ ndi kumuika m’matangadza+ amene anali pa Chipata Chakumtunda cha Benjamini, cha m’nyumba ya Yehova. Yohane 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atanena zimenezi, mmodzi wa alonda amene anaimirira chapafupi anamenya Yesu mbama,+ ndi kunena kuti: “Ungamuyankhe choncho wansembe wamkulu?”
24 Tsopano Zedekiya mwana wa Kenaana anayandikira Mikaya ndipo anam’menya mbama,+ n’kunena kuti: “Kodi mzimu wa Yehova wachoka bwanji kwa ine n’kukalankhula ndi iwe?”+
2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya+ ndi kumuika m’matangadza+ amene anali pa Chipata Chakumtunda cha Benjamini, cha m’nyumba ya Yehova.
22 Atanena zimenezi, mmodzi wa alonda amene anaimirira chapafupi anamenya Yesu mbama,+ ndi kunena kuti: “Ungamuyankhe choncho wansembe wamkulu?”