26 ‘Yehova wakuika kukhala wansembe m’malo mwa Yehoyada wansembe kuti ukhale woyang’anira wamkulu m’nyumba ya Yehova+ ndi kuti umange munthu aliyense wamisala+ amene akuchita zinthu ngati mneneri. Munthu woteroyo umuike m’matangadza, miyendo, manja ndi mutu womwe.+