2 Mbiri 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mukawauze kuti, ‘Mfumu yanena kuti: “Kam’tsekereni munthu uyu.+ Muzim’patsa chakudya chochepa+ ndi madzinso ochepa, kufikira ine nditabwerera mu mtendere.”’”+ Mlaliki 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa mawu a mfumu ali ndi mphamvu yolamulira,+ ndipo ndani angaifunse kuti: ‘Kodi mukuchita chiyani?’”
26 Mukawauze kuti, ‘Mfumu yanena kuti: “Kam’tsekereni munthu uyu.+ Muzim’patsa chakudya chochepa+ ndi madzinso ochepa, kufikira ine nditabwerera mu mtendere.”’”+
4 chifukwa mawu a mfumu ali ndi mphamvu yolamulira,+ ndipo ndani angaifunse kuti: ‘Kodi mukuchita chiyani?’”