Salimo 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usapse mtima ndipo pewa kukwiya.+Usapse mtima kuti ungachite choipa.+ Salimo 141:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+ Miyambo 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wokonda kukwiya amayambitsa mkangano,+ ndipo aliyense wokonda kupsa mtima amakhala ndi machimo ambiri.+ Agalatiya 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko,
5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+
22 Munthu wokonda kukwiya amayambitsa mkangano,+ ndipo aliyense wokonda kupsa mtima amakhala ndi machimo ambiri.+
20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko,