Miyambo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usadzudzule wonyoza kuti angadane nawe.+ Dzudzula munthu wanzeru ndipo adzakukonda.+ Miyambo 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Menya wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere.+ Ndipo womvetsa zinthu uyenera kum’dzudzula kuti adziwe zinthu zowonjezereka.+ Miyambo 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera, amakhala ngati ndolo* yagolide, ndiponso ngati chokongoletsera chagolide wapadera.+
25 Menya wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere.+ Ndipo womvetsa zinthu uyenera kum’dzudzula kuti adziwe zinthu zowonjezereka.+
12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera, amakhala ngati ndolo* yagolide, ndiponso ngati chokongoletsera chagolide wapadera.+