Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 22:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Poyankha, mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Pali munthu mmodzi amene tingathe kufunsira kwa Yehova kudzera mwa iye,+ koma ineyo ndimadana naye kwambiri,+ chifukwa salosera zabwino zokhudza ine, koma zoipa.+ Munthuyo dzina lake ndi Mikaya mwana wa Imula.” Koma Yehosafati anati: “Musalankhule choncho mfumu.”+

  • Miyambo 15:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu wonyoza amadana ndi munthu amene akum’dzudzula.+ Iye sadzapita kwa anthu anzeru.+

  • Miyambo 23:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Usalankhule m’makutu mwa munthu wopusa,+ chifukwa iye adzanyoza mawu ako anzeru.+

  • Mateyu 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Musamapatse agalu zinthu zopatulika,+ kapena kuponyera nkhumba ngale zanu, kuopera kuti zingapondeponde ngalezo+ kenako n’kutembenuka ndi kukukhadzulani.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena