Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Poyankha, mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati+ kuti: “Pali munthu mmodzi+ amene tingathe kufunsira kwa Yehova kudzera mwa iye, koma ineyo ndimadana naye+ kwambiri, chifukwa masiku ake onse salosera zabwino zokhudza ine, koma zoipa zokhazokha.+ Munthuyo dzina lake ndi Mikaya mwana wa Imula.”+ Koma Yehosafati anati: “Musalankhule choncho mfumu.”+

  • Yesaya 30:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+

  • Yeremiya 38:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo akalonga anayamba kuuza mfumu kuti: “Chonde lolani kuti munthu uyu aphedwe,+ chifukwa iye akufooketsa amuna ankhondo amene atsala mumzinda uno, pamodzi ndi anthu onse, mwa kuwauza mawu amenewa.+ Munthu ameneyu sakuwafunira mtendere anthuwa, koma akuwafunira tsoka.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena