Miyambo 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera, amakhala ngati ndolo* yagolide, ndiponso ngati chokongoletsera chagolide wapadera.+ Mika 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Inu a nyumba ya Yakobo,+ kodi mukunena kuti: “Kodi mzimu wa Yehova sukukhutira, kapena kodi izi ndiye zochita zake?”+ Kodi mawu anga sapindulitsa+ munthu woyenda mowongoka mtima?+
12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera, amakhala ngati ndolo* yagolide, ndiponso ngati chokongoletsera chagolide wapadera.+
7 “‘Inu a nyumba ya Yakobo,+ kodi mukunena kuti: “Kodi mzimu wa Yehova sukukhutira, kapena kodi izi ndiye zochita zake?”+ Kodi mawu anga sapindulitsa+ munthu woyenda mowongoka mtima?+