Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Salimo 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti mawu a Yehova ndi owongoka,+Ndipo ntchito zake zonse ndi zodalirika.+ Yeremiya 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+ Mawu anu amandikondweretsa+ ndi kusangalatsa mtima wanga,+ pakuti ine ndimatchedwa ndi dzina lanu,+ inu Yehova Mulungu wa makamu.+
7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+ Mawu anu amandikondweretsa+ ndi kusangalatsa mtima wanga,+ pakuti ine ndimatchedwa ndi dzina lanu,+ inu Yehova Mulungu wa makamu.+