Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 119:72
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  72 Chilamulo+ chotuluka pakamwa panu n’chabwino kwa ine,+

      N’chabwino kwambiri kuposa ndalama masauzande zagolide ndi zasiliva.+

  • Mateyu 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Musaganize kuti ndinabwera kudzawononga Chilamulo+ kapena Zolemba za aneneri. Sindinabwere kudzaziwononga koma kudzazikwaniritsa.+

  • Luka 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Komanso, masiku akuti iwo ayeretsedwe+ malinga ndi chilamulo cha Mose atakwanira, anapita naye ku Yerusalemu kukam’pereka kwa Yehova.

  • Aroma 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pajatu akumva chabe chilamulo si amene amakhala olungama pamaso pa Mulungu, koma otsatira+ chilamulo ndiwo adzayesedwa olungama.+

  • Aroma 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti tikudziwa kuti Chilamulo n’chauzimu,+ koma ine ndine wakuthupi, wogulitsidwa ku uchimo.+

  • Aroma 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mumtima mwanga+ ndimasangalala kwambiri+ ndi chilamulo cha Mulungu,

  • Aroma 9:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Koma ngakhale kuti Aisiraeli anali kutsatira lamulo la chilungamo, sanalipeze lamulolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena