Luka 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso nthawi yoti iwo ayeretsedwe mogwirizana ndi Chilamulo cha Mose itakwana,+ anapita ndi mwanayo ku Yerusalemu kukamupereka kwa Yehova.* Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:22 Yesu—Ndi Njira, tsa. 20 Tsanzirani, ptsa. 160-161 Nsanja ya Olonda,10/1/2008, tsa. 25 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Yesu anakamupereka kwa Yehova kukachisi (gnj 1 43:56–45:02)
22 Komanso nthawi yoti iwo ayeretsedwe mogwirizana ndi Chilamulo cha Mose itakwana,+ anapita ndi mwanayo ku Yerusalemu kukamupereka kwa Yehova.*