Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mkazi akakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa kwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira pa nthawi imene akusamba.+

  • Levitiko 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mkaziyo azipitiriza kudziyeretsa ku magazi ake kwa masiku enanso 33. Asamakhudze chilichonse chopatulika komanso asamalowe mʼmalo oyera mpaka atakwanitsa masiku a kuyeretsedwa kwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena