Levitiko 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kwa masiku enanso 33, mkaziyo azikhala panyumba kuti ayeretsedwe ku magazi ake. Asakhudze chilichonse chopatulika, ndipo asalowe m’malo oyera, kufikira masiku a kuyeretsedwa kwake atakwanira.+
4 Kwa masiku enanso 33, mkaziyo azikhala panyumba kuti ayeretsedwe ku magazi ake. Asakhudze chilichonse chopatulika, ndipo asalowe m’malo oyera, kufikira masiku a kuyeretsedwa kwake atakwanira.+