Luka 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso, masiku akuti iwo ayeretsedwe+ malinga ndi chilamulo cha Mose atakwanira, anapita naye ku Yerusalemu kukam’pereka kwa Yehova.
22 Komanso, masiku akuti iwo ayeretsedwe+ malinga ndi chilamulo cha Mose atakwanira, anapita naye ku Yerusalemu kukam’pereka kwa Yehova.