Agalatiya 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Sindikukankhira kumbali kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ chifukwa ngati munthu amakhala wolungama kudzera mwa chilamulo,+ ndiye kuti Khristu anangofa pachabe.+ Agalatiya 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inuyo amene mukufuna kuyesedwa olungama mwa chilamulo, mwadzilekanitsa ndi Khristu,+ kaya mukhale ndani, mwagwera kunja kwa kukoma mtima kwake kwakukulu.+
21 Sindikukankhira kumbali kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ chifukwa ngati munthu amakhala wolungama kudzera mwa chilamulo,+ ndiye kuti Khristu anangofa pachabe.+
4 Inuyo amene mukufuna kuyesedwa olungama mwa chilamulo, mwadzilekanitsa ndi Khristu,+ kaya mukhale ndani, mwagwera kunja kwa kukoma mtima kwake kwakukulu.+