Aroma 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero pamaso pake palibe munthu amene adzayesedwe wolungama+ mwa ntchito za chilamulo,+ popeza chilamulo chimachititsa kuti tidziwe uchimo molondola.+ Aroma 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa munthu amene wagwira ntchito+ saona malipiro ake ngati kukoma mtima kwakukulu,+ koma ngati ngongole.+ Aroma 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma ngakhale kuti Aisiraeli anali kutsatira lamulo la chilungamo, sanalipeze lamulolo.+
20 Chotero pamaso pake palibe munthu amene adzayesedwe wolungama+ mwa ntchito za chilamulo,+ popeza chilamulo chimachititsa kuti tidziwe uchimo molondola.+
4 Chifukwa munthu amene wagwira ntchito+ saona malipiro ake ngati kukoma mtima kwakukulu,+ koma ngati ngongole.+