Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiye kodi chinthu chabwino chinakhala imfa kwa ine? Ayi ndithu! Koma uchimo ndiwo unakhala imfa kwa ine, kuti uonekere kuti ndi umene ukubala imfa mwa ine kudzera m’chinthu chabwinocho,+ kuti kudzera m’malamulo, uchimowo uonekere kuti ndi woipa kwambiri.+

  • Agalatiya 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nanga tsopano Chilamulo chinakhalapo chifukwa chiyani? Anachiwonjezerapo kuti machimo aonekere,+ mpaka amene ali mbewuyo atafika,+ amene anapatsidwa lonjezolo. Ndipo Chilamulocho chinaperekedwa kudzera mwa angelo,+ kudzeranso m’dzanja la mkhalapakati.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena