Salimo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’zolakalakika kuposa golide, kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+N’zotsekemera* kuposa uchi,+ inde kuposa uchi umene ukukha m’zisa.+ Salimo 119:127 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 127 N’chifukwa chake ine ndimakonda malamulo anu+Kuposa golide, golide woyenga bwino.+ Miyambo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’zamtengo wapatali kuposa miyala ya korali,+ ndipo zonse zimene umakonda sizingafanane nazo. Miyambo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+
10 N’zolakalakika kuposa golide, kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+N’zotsekemera* kuposa uchi,+ inde kuposa uchi umene ukukha m’zisa.+
10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+