Salimo 119:127 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 127 N’chifukwa chake ine ndimakonda malamulo anu+Kuposa golide, golide woyenga bwino.+ Miyambo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+
10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+