Salimo 119:103 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 103 Mawu anu amatsekemera m’kamwa mwanga,Kuposa mmene uchi umakomera!+ Miyambo 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mawu okoma ali ngati chisa cha uchi.+ Amakhala okoma kwa munthu ndipo amachiritsa mafupa.+