Miyambo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zimenezi zidzachiritsa+ mchombo wako ndi kutsitsimutsa mafupa ako.+ Miyambo 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti izo ndi moyo kwa amene amazipeza+ ndiponso ndi thanzi labwino kwa thupi lawo lonse.+ Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+ Miyambo 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mtima wosangalala ndiwo mankhwala ochiritsa,+ koma mtima wosweka umaumitsa mafupa.+
18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+