Salimo 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mphamvu yanga yauma gwaa, ngati phale.+Lilime langa lamamatira kunkhama zanga,+Ndipo mwandikhazika m’fumbi la imfa.+ Miyambo 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mtima wa munthu ukhoza kupirira matenda,+ koma mtima wosweka ndani angaupirire?+ 2 Akorinto 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kumva chisoni mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu kumachititsa munthu kulapa ndi kupeza chipulumutso, zimene munthu sangadandaule nazo.+ Koma chisoni cha dziko chimabweretsa imfa.+
15 Mphamvu yanga yauma gwaa, ngati phale.+Lilime langa lamamatira kunkhama zanga,+Ndipo mwandikhazika m’fumbi la imfa.+
10 Kumva chisoni mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu kumachititsa munthu kulapa ndi kupeza chipulumutso, zimene munthu sangadandaule nazo.+ Koma chisoni cha dziko chimabweretsa imfa.+