Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 n’kuyamba kunena kuti:

      “Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+

      Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+

      Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+

      Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+

  • 2 Akorinto 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Choncho sitikubwerera m’mbuyo. Koma ngakhale munthu wathu wakunja akutha, ndithudi munthu wathu wamkati+ akukhalitsidwanso watsopano tsiku ndi tsiku.

  • 2 Akorinto 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chotero ndimasangalala ndi kufooka, zitonzo, zosowa zanga, mazunzo ndi zovuta zina, chifukwa cha Khristu. Pakuti pamene ndili wofooka, m’pamene ndimakhala wamphamvu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena