Yobu 31:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi amene anandipanga m’mimba si amene anapanganso iyeyo?+Kodi si mmodzi yemweyo amene anatipanga tonsefe m’mimba? Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+ Mlaliki 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Monga mmene munthu anabadwira kuchokera m’mimba mwa mayi ake, adzapitanso wamaliseche+ ngati mmene anabwerera, ndipo palibe chilichonse chimene adzatenge+ pa ntchito yake imene anaigwira mwakhama. 1 Timoteyo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti sitinabwere ndi kanthu m’dziko, ndipo sitingatulukemo ndi kanthu.+
15 Kodi amene anandipanga m’mimba si amene anapanganso iyeyo?+Kodi si mmodzi yemweyo amene anatipanga tonsefe m’mimba?
15 Monga mmene munthu anabadwira kuchokera m’mimba mwa mayi ake, adzapitanso wamaliseche+ ngati mmene anabwerera, ndipo palibe chilichonse chimene adzatenge+ pa ntchito yake imene anaigwira mwakhama.