Salimo 49:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti pa imfa yake sangatenge kena kalikonse.+Ulemerero wake sudzapita naye pamodzi.+ Luka 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako adzaufuna.+ Nanga chuma chimene waunjikachi chidzakhala cha ndani?’+ 1 Timoteyo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti sitinabwere ndi kanthu m’dziko, ndipo sitingatulukemo ndi kanthu.+
20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako adzaufuna.+ Nanga chuma chimene waunjikachi chidzakhala cha ndani?’+