Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 n’kuyamba kunena kuti:

      “Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+

      Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+

      Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+

      Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+

  • Mlaliki 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Monga mmene munthu anabadwira kuchokera m’mimba mwa mayi ake, adzapitanso wamaliseche+ ngati mmene anabwerera, ndipo palibe chilichonse chimene adzatenge+ pa ntchito yake imene anaigwira mwakhama.

  • Luka 12:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako adzaufuna.+ Nanga chuma chimene waunjikachi chidzakhala cha ndani?’+

  • 1 Timoteyo 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena