Maliko 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yesu anayang’ana uku ndi uku, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Zidzakhalatu zovuta kwambiri kuti anthu andalama+ adzalowe mu ufumu wa Mulungu!”+
23 Yesu anayang’ana uku ndi uku, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Zidzakhalatu zovuta kwambiri kuti anthu andalama+ adzalowe mu ufumu wa Mulungu!”+