Salimo 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndidzatamanda Yehova nthawi zonse.+Ndidzamutamanda ndi pakamwa panga mosalekeza.+ Danieli 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anati: “Dzina la Mulungu likhale lotamandika+ kuyambira kalekale mpaka kalekale, pakuti nzeru ndi mphamvu ndi zake.+
20 Iye anati: “Dzina la Mulungu likhale lotamandika+ kuyambira kalekale mpaka kalekale, pakuti nzeru ndi mphamvu ndi zake.+