Salimo 44:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tidzayamika Mulungu nthawi zonse,+Tidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale.+ [Seʹlah.] Salimo 71:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’kamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu,+Ndipo pakamwa panga pakunena za ulemerero wanu tsiku lonse.+
8 M’kamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu,+Ndipo pakamwa panga pakunena za ulemerero wanu tsiku lonse.+