Salimo 71:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼkamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu.+Tsiku lonse ndimanena za ulemerero wanu.