Salimo 35:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Lilime langa linene chapansipansi za chilungamo chanu,+Ndipo likutamandeni tsiku lonse.+ Salimo 145:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzakutamandani tsiku lonse.+Ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+