Salimo 51:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, tsegulani milomo yangayi,+Kuti pakamwa panga patamande inu.+ Salimo 145:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakamwa panga padzalankhula zotamanda Yehova,+Ndipo anthu onse atamande dzina lake loyera mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+
21 Pakamwa panga padzalankhula zotamanda Yehova,+Ndipo anthu onse atamande dzina lake loyera mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+