Mateyu 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uthenga wabwino+ uwu wa ufumu+ udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni ku mitundu yonse,+ kenako mapeto+ adzafika. Aroma 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ngati ukulengeza kwa anthu ‘mawu amene ali m’kamwa mwakowo,’+ akuti Yesu ndiye Ambuye,+ ndipo mumtima mwako ukukhulupirira kuti Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ udzapulumuka.+
14 Uthenga wabwino+ uwu wa ufumu+ udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni ku mitundu yonse,+ kenako mapeto+ adzafika.
9 Pakuti ngati ukulengeza kwa anthu ‘mawu amene ali m’kamwa mwakowo,’+ akuti Yesu ndiye Ambuye,+ ndipo mumtima mwako ukukhulupirira kuti Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ udzapulumuka.+