Salimo 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndidzatamanda Yehova nthawi zonse.+Ndidzamutamanda ndi pakamwa panga mosalekeza.+ Salimo 71:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’kamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu,+Ndipo pakamwa panga pakunena za ulemerero wanu tsiku lonse.+ Salimo 109:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzatamanda kwambiri Yehova ndi pakamwa panga,+Ndipo ndidzamutamanda pakati pa anthu ambiri.+ Salimo 145:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakamwa panga padzalankhula zotamanda Yehova,+Ndipo anthu onse atamande dzina lake loyera mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+
8 M’kamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu,+Ndipo pakamwa panga pakunena za ulemerero wanu tsiku lonse.+
21 Pakamwa panga padzalankhula zotamanda Yehova,+Ndipo anthu onse atamande dzina lake loyera mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+