Yobu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 nʼkunena kuti: “Ndinatuluka mʼmimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,Ndipo ndidzabwerera ndilinso wamaliseche.+ Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga. Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.” Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:21 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,8/15/2006, tsa. 223/15/2006, tsa. 14
21 nʼkunena kuti: “Ndinatuluka mʼmimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,Ndipo ndidzabwerera ndilinso wamaliseche.+ Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga. Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”