Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzadya chakudya kuchokera mʼthukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, chifukwa nʼkumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+ Salimo 49:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa akadzamwalira sadzatenga china chilichonse.+Ulemerero wake sadzapita nawo limodzi.+ Mlaliki 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Monga mmene munthu anabadwira kuchokera mʼmimba mwa mayi ake, adzapitanso wamaliseche ngati mmene anabwerera.+ Ndipo sangatenge chilichonse pa ntchito yake imene anaigwira mwakhama.+ Mlaliki 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu* udzabwerera kwa Mulungu woona amene anaupereka.+ 1 Timoteyo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pajatu sitinabwere ndi kanthu mʼdziko ndipo sitingachokemo ndi kanthu.+
19 Udzadya chakudya kuchokera mʼthukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, chifukwa nʼkumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+
15 Monga mmene munthu anabadwira kuchokera mʼmimba mwa mayi ake, adzapitanso wamaliseche ngati mmene anabwerera.+ Ndipo sangatenge chilichonse pa ntchito yake imene anaigwira mwakhama.+
7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu* udzabwerera kwa Mulungu woona amene anaupereka.+