Yobu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 nʼkunena kuti: “Ndinatuluka mʼmimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,Ndipo ndidzabwerera ndilinso wamaliseche.+ Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga. Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.” Salimo 49:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Musachite mantha chifukwa chakuti munthu wina walemera,Kapena chifukwa chakuti katundu wamʼnyumba mwake wawonjezeka,17 Chifukwa akadzamwalira sadzatenga china chilichonse.+Ulemerero wake sadzapita nawo limodzi.+
21 nʼkunena kuti: “Ndinatuluka mʼmimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,Ndipo ndidzabwerera ndilinso wamaliseche.+ Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga. Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”
16 Musachite mantha chifukwa chakuti munthu wina walemera,Kapena chifukwa chakuti katundu wamʼnyumba mwake wawonjezeka,17 Chifukwa akadzamwalira sadzatenga china chilichonse.+Ulemerero wake sadzapita nawo limodzi.+