Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kaini atamva zimenezi anadandaulira Yehova kuti: “Chilango cha kulakwa kwanga n’chachikulu kwambiri moti sindingathe kuchipirira.

  • Mateyu 27:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho iye anaponya ndalama zasiliva zija m’kachisi n’kuchoka, ndipo anakadzimangirira.+

  • Aheberi 12:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mukudziwa kuti pambuyo pake, atafunanso kulandira dalitso monga cholowa chake,+ anamukanira.+ Pakuti ngakhale kuti anayesetsa ndi mtima wonse, kwinaku akugwetsa misozi,+ kuti bambo ake asinthe maganizo, sizinatheke.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena