Aheberi 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mukudziwa kuti pambuyo pake, pamene ankafuna kulandira madalitso,* anamukanira. Ngakhale kuti anayesetsa ndi mtima wonse kwinaku akulira,+ kuti bambo ake asinthe maganizo, sizinatheke.
17 Mukudziwa kuti pambuyo pake, pamene ankafuna kulandira madalitso,* anamukanira. Ngakhale kuti anayesetsa ndi mtima wonse kwinaku akulira,+ kuti bambo ake asinthe maganizo, sizinatheke.