Genesis 27:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iyenso anakonzera bambo ake nyama ija mopatsa madyo. Kenako anapita nayo kwa bambo ake n’kuwauza kuti: “Bambo, dzukani mudye nyama imene ndakupherani ine mwana wanu, kuti mundidalitse.”+
31 Iyenso anakonzera bambo ake nyama ija mopatsa madyo. Kenako anapita nayo kwa bambo ake n’kuwauza kuti: “Bambo, dzukani mudye nyama imene ndakupherani ine mwana wanu, kuti mundidalitse.”+