Genesis 27:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno Isaki, bambo ake, anati: “Nanga iwenso ndiwe ndani?” Ndipo iye anayankha kuti: “Ndine mwana wanu, mwana wanu woyamba Esau.”+
32 Ndiyeno Isaki, bambo ake, anati: “Nanga iwenso ndiwe ndani?” Ndipo iye anayankha kuti: “Ndine mwana wanu, mwana wanu woyamba Esau.”+