Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 17:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma Ahitofeli ataona kuti malangizo ake sanawagwiritse ntchito,+ anakwera bulu wake ndi kunyamuka kupita kunyumba yake kumzinda wakwawo.+ Kenako anakonzekeretsa banja lake+ ndipo anadzimangirira+ moti anafa.+ Chotero anaikidwa m’manda+ a makolo ake.

  • Salimo 55:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+

      Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+

      Koma ine ndidzakhulupirira inu.+

  • Machitidwe 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 (Chotero munthu ameneyu, anagula+ munda ndi malipiro a ntchito zosalungama.+ Anagwa chamutu+ n’kuphulika mimba, moti phokoso la kuphulikako linamveka, ndipo matumbo ake onse anakhuthuka.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena