Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Usaphe munthu.*+

  • 1 Samueli 31:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako Sauli anauza womunyamulira zida kuti: “Solola lupanga lako+ undibaye* nalo, kuti amuna osadulidwawa+ asandipeze ndi kundibaya komanso kundizunza.” Koma womunyamulira zida uja sanafune,+ chifukwa anali kuopa kwambiri. Chotero Sauli anatenga lupanga lake ndi kuligwera.+

  • 1 Mafumu 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Zimiri atangoona kuti mzindawo walandidwa, anakalowa munsanja yomwe inali panyumba ya mfumu n’kuyatsa nyumbayo iye ali mkati mwake, moti anafera momwemo.+

  • Mateyu 27:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho iye anaponya ndalama zasiliva zija m’kachisi n’kuchoka, ndipo anakadzimangirira.+

  • Machitidwe 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 (Chotero munthu ameneyu, anagula+ munda ndi malipiro a ntchito zosalungama.+ Anagwa chamutu+ n’kuphulika mimba, moti phokoso la kuphulikako linamveka, ndipo matumbo ake onse anakhuthuka.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena