Mateyu 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho iye anaponya ndalama zasiliva zija m’kachisi n’kuchoka, ndipo anakadzimangirira.+